Home learning (Nyanja)

£0.00

Double-sided A2 poster.

Published by EENET and NAD, 2020

49 in stock

Category:

Description

Nanga chithunzi ichi ndicha ndani?

  • Chithunzi ichi ndicha mabanja onse ali na ana olemala na osalemala.
  • Ndi cha aliyense – amayi ndi abambo, osamalira, ana, achinyamata, abale, agogo ndi ambuya, amalume ndi azakhali …

Nanga chithunzi ichi ndicha chiyani?

Chimankala chovuta ngati masukulu banavala komanso ana ali panyumba. Bakulu bamafuna kuthandiza ana ndi achinyamata kuti apunzire mwamene apunzirira ku sukulu, koma nichovuta.

Chithunzi ichi chikuwonetsa njira zambiri mabanja akupunzirira kudala kunyumba. Aliyense akonza kugwiritsa nchito malingaliro ake nakupanga zina njira izi zopunzirira.

Nanga nichiyani chitunzi ichi chinapangidwa?

Chithunzi ichi chitandiza mabanja kudziba mwamene kupunzira kumachitikira kunyumba na mwamene kupunzira kunyumba kungatandizire kusintha kupunzira kusukulu na mdera.

Mwamene mungagwiritsire nchito chitunzi ichi?

  • Ikani chithunzi ichi pakhoma lanu kuti aliyense mubanja azikwanisa kuchiwona. Funsani ana kuti atandizire kusanka pamene mungayike chitunzi ichi.
  • Yanganani pa chitunzi ichi ntawi iliyonse.
  • Ganizirani za zitunzi izi. Niziti zitunzi zamene mumakonda kuyangana kwambiri?
  • Mwawona chiyani? Muganiza kuti nichani chamene chichitika muzitunzi izi?
  • Chimupasani malingaliro bwanji wopunzirira kunyumba?
  • Palibe mayanko yabwino kapena yoyipa.

Additional information

Weight 0.045 kg
Dimensions 0.3 × 21 × 29.7 cm

Reviews

There are no reviews yet.

Be the first to review “Home learning (Nyanja)”

Your email address will not be published.